Paroles de John chilembwe remix

Revolver

pochette album John chilembwe remix
Voir sur Itunes

sonnerie téléphone portable pour John chilembwe remix

Verse 1:
(krazie g)
Fans ndimaibanda ngati ganja ndikupotayi
Ndili nayo yambirimbiri ili nthumba mwa 3 quarter'yi
(ah iwe sitikukamba zimenezo) eish oh ayi
(tikukamba za chilembwe) oh n'dala wa botayi
Ndimamusaka ngati azungu amene anamupha
Ndikampeza celebration pali ponse kudumphadumpha
Ndimayesesa daily apezeke nthumbamu
Nde dolla zosaka ku lilongwe kuchita kutuwa mbu
I want ronaldo, messi money, nike, addidas
Ngati ili nkhani ya dollar ndipange add basi
Make mad thousands and call em crazy g's
I make crazy millions and call em amazing me
Ndikudya paper koma akumva kuwawa ndi wina
Ndikudya esther lero koma mawa ndi tina
Siine wama looks ndine nkhwangwa
Koma akazi ndi nkhuni ndimaawaza
Chifukwa cha chilembwe wanga

(revolver)
Ndikusaka m'busa uja in a khakhi suit
If you see him chonde mundiwuze ali kuti
No homo but i love him like a choir
Sindigwanda chilembwe olo atakhala
Wakale, wokwinyika ngakhale wong'ambika
Olo ali wonyowa ine ndimuyanika
Sinditha kuphika but damn ndikuphula
Funsa mng'ono wa bebi yanga, ndikudya moola
Coz i stay on my grind like am s'possed to
Kufuna jc ngati ndili mu form 2
Thats john chilembwe, mng'ono wa kamuzu
Mkulu wa gomani, best friend wanga uyu
Ngongole sindibweza, ndikasanja ndimasowa
Mzinda wandikwana ndikulowela ku dowa
Alipo ambiri ma man onditchesa
Lero akafika pa yard sandipeza
Ndikuteteza

Chorus:
(tanaposi & krazie g)
John chilembwe
John chilembwe
Jo-jo john chilembwe
John chilembwe
Amapoilira john chilembwe uyu
Akupoilira john chilembwe

Verse 2:
(martse)
Ma heroe ndimaasaka john chilembwe ndiwoyamba
And now i'm switching gears nduhasa kamuzu banda
Having money is an option all i had to do is choose
Sindimalamulidwa nde sindikhala mmaluzi
This aint no lie
John chilembwe wako ngwa china, wameta mohawk, wavala tie
Wa ine ndi brand new for zibagi, dubai
Ndine tholo ndi kale nde ndimangokhala high
Martse ndi mfana wotentha nde palibe akuti nyo
Ndine mtumbuka wosamba mphwanga, you already know
Nde mukamakambakamba za john chilembweyo
Waine ali ngati dstv, so much more
You dig

(hypa)
Dolla zanga ndizama looks ndiyeno fans imangokongola
Fans yakunyasa imabwela kuzangokongola
Dolla zimathoka koma ine ndili phe
Iwe zako kungothoka uwone tulo ndiliphe
Ndikufuna kunenepa nde ndikungodya zi money
Ku chipatala andiwuza ndizidya ndisazimane
Kuthoka ndi chilembwe timatchila mwa kathithi
Ngati dolla zimathoka iwe zako nzachibwibwi
I'm sick with the money dolla zanga zingofwenthila
Ndinkona ndimaziblowa ndikazimva zikufwenthila
Anijo kundiyabwa ndimangokanda ngati bongo man
Koma kundipempha ndimangokana ngati ntaba man
Nkhani za chilembwezi zilibe chibale
Olo faith zamakwachazi alibe chibale
Dolla zanga zimathokadi, zimapanga noise
Iwe zako kusokosa ndekuti wagwetsa ma coins
(back to chorus)

Verse 3:(judagaga)
I keep it old school, john chilembwe yekha yekha
Kamuzu ali bho koma nthumba akumachepa
Ndikasanja dolla ndimafuna fans idziwe
Mahope n'nawathoka kuti nawonso adiwe
Get his face on a bank note nde ndizamulora
Dead people got my number coz dolla zikundikhola
I get money by all means even change chaku msika
Chilling with dead people thats why my flow is mad sicker
Ndimamukonda john chilembwe, you can call me haida
Cause when i have him in my pockets i'm sipping ciders
In love with this black man in a khakhi suit
Siine mzungu koma nane ndimamuhanta ndi mifuti
My account got much figure kuposa akazi
Dirty money yaku malawi, john chilembwe wa magazi
Get my money in my bra ngati recka sungandibele
Ndimazakuwa kuti huh nanenso ndizamufele
(back to chorus)

Les autres musiques de Revolver