Paroles de Zoononga moyo

Kbg

pochette album Zoononga moyo
Voir sur Itunes

sonnerie téléphone portable pour Zoononga moyo

Verse 1:lawi
Amati bawa
Ndi njira yochotsela nkhawa
Nanga bwanji ukadzuka mmawa
Matsile maluzi uliso confused
Ndingonena chindunji
Chenicheni nchiti
Chokhalila mfiti
When in actual sense you r a slave to the sin that yo glue to
Iwe tchimo litavala umunthu
Chonde ndithandizeni
Ndidziweko swaga as much as i know ndizoononga moyo wanga
Sikuzikweza kodi?
Kuwalila kodi?
Kukhutitsidwa ndimmene ndavalila kodi?
Inde asungwana apapa mukukhwana titha kuyamikila mpakana kupanga mwana
Inde abwana mwatchena osanama but check on the . . . ndiyesu mwasemphana
U can be who u want to b
Multiply zinthu ngati tyms
U can buy evrything with paper
But heaven uuuh uuuh zachisoni pepa

(chorus:)
Kodi wapindulanji iweyo
Utapeza zonse zofuna mtima wako
Koma zonse zomwe wapezazo
Mulibe chipulumutso
Ndizinthu zoonona moyo wako x2

Verse2:kbg
Lawi nane ndiwauze fanzi
. . . .

Les autres musiques de Kbg