Il testo della Malawi native anthem text

National Anthem

pochette album Malawi native anthem text
Vista su itunes

sonnerie téléphone portable pour Malawi native anthem text

1.
Mlungu dalitsani malawi,
Mumsunge m'mtendere.
Gonjetsani adani onse,
Njala, nthenda, nsanje.
Lunzitsani mitima yathu,
Kuti tisaope.
Mdalitse mtsogo leri na fe,
Ndi mai malawi.
2.
Malawi ndziko lokongola,
La chonde ndi ufulu,
Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri,
Ndithudi tadala.
Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,
N'mphatso zaulere.
Nkhalango, madambo abwino.
Ngwokoma malawi.
3.
O! ufulu tigwirizane,
Kukweza malawi.
Ndi chikondi, khama, kumvera,
Timutumikire.
Pa nkhondo nkana pa mtendere,
Cholinga n'chimodzi.
Mai, bambo, tidzipereke,
Pokweza malawi.
Sent by carlos andr pereira da silva branco

Altri brani di National Anthem