Il testo della Waku blantyre
Revolver
Verse 1(chavura)
Mu b town ndimafila life (life)
Aliyense oyimba ndi ine ndimakiller guys (guys)
Ndikamalemba verse ndimatcheka line up (up)
Kuyisiya fans m'madzi ngati pine appl'
Ndimazisata amathoka shit (shit)
Amasata nkhani zanga ndikasoka chick (chick)
Mafanawa pa internet amandistokadi
Akandipeza amandifunsa, amandibowadi
Zowonadinso mafanawa simachita show (show)
Ronald'nso nyimbo zawo samamixer bho (bho)
Tawonaninso achina volver amangoakhilanso
Amafuna atandibula ngati filabo
Pozandibula azafila bho (bho)
Ngati chick yopanda mbina sazachithako(ko)
Chino ndichiakita mfana sazachiphako(ko)
Wake ndadya koma wanga sazachi... ha
Chorus(stich fray)
(kuyenda
Ntown) aliyense maso pa ine,amene
Samandiziwa angoti uje bwanji
(ndiyende ntown) aliyense maso pa
Ine,amene samandidziwa angoti uje
Bwanji
Amene amandiziwa akuti ndine dolo
Amene amandiziwa akuti ndine shasha
Amene amandiziwa akuti ndine dolo
Amandifila fukwa ndine waku blantyre
Verse 2(revolver)
Akuti volver timakufila ku mponela
Nyimbo zanyuwanizo muzitiponyela
Achina mbina mbina muziti ponyela
Ndikutentha mahater sakuwothela
Amanditcha austin, mfana wa powers
Osati movie, ndikuthoka za bawazi
Green ndimamwa, mu tracks ndimamudya
Akuti ndi mfumu komabe ndimamuda
Get it, musamude fumu-lani
Stich andifunsa 'iwe volver uku-tani
Zomapanga beef suzatukuka nazo
Olo utahitter sakutenga kuma show'
Neighbour wanga akuboweka
Sandiziwa koma nyimbo zanga akuloweza
Speakers on blast, chifisi pa repeat
Ine nditachokapo kubwela round six
(chorus)
Verse 3 (stich fray)
Yeah,them wan fi follow me ina real
Life
But mi so tweeter me forget & mi
Nah follow back
Amati hater koma
Chonsecho amatifila
Ngati ma chick awo athetsa amatilira
Check it afuna
Khalangati ifedi,
Kuzimva u landlord mu
Gameyi koma ali pa rent (ha ha ha ha)
,
Ndima students ozimva u head,
Ratatatatatata,stichfray ndinedi
Ndinedi dolo
Amene amandiziwa akuti ndine shasha
Amene amandiziwa akuti ndine dolo
Mukut
Sim'mandiziwa pamene ndimakubowani
(chorus 2x)
Altri brani di Revolver
2.a.m. big wish
Revolver

49 states
Revolver

A song she wrote
Revolver

Il testo della Back to you
Revolver
Bagi party
Revolver

Balulalow
Revolver

Birds in dm
Revolver

Il testo della Brothers
Revolver

Calm down
Revolver

Cassavetes
Revolver
Chikondi chathu
Revolver

Il testo della Do you have a gun ?
Revolver

El roce de tu piel
Revolver

Get around town
Revolver
Have you seen my new friends
Revolver

Il testo della It's alright
Revolver
John chilembwe remix
Revolver

Leave me alone
Revolver

Let go
Revolver

Il testo della Let's get together
Revolver
L.j.b.f (lets just be friends)
Revolver

Losing you
Revolver

Luke, mike & john
Revolver

Il testo della My lady i
Revolver

My old self
Revolver
Ndiwe number one
Revolver
Never khuzed
Revolver

Il testo della Parallel lives
Revolver
Parallel lives (traduction)
Revolver

San pedro
Revolver
Il testo della canzone waku blantyre da revolver.




